Lyrics.com »

Search results for 'Zonsé'

Yee yee! We've found 92 lyrics matching Zonsé.

Year:


Filter by gender:

Lyrics:

chasefukira
Moyo wanga unasintha
Mtima wanga kuyamika
Ndizovuta kunena
M'mene m'mandikondera
Mwandimasula ku nsinga
Mtima wanga kuyamika

Ndinu zonse zanga
anu  anangochoka alamu anu

Ayiwala zonse, tinakambilana zija
Ayiwala zonse, tinalambilana zina eish

Ayiwala zonse, ndinawapangila zija
Ayiwala zonse
tikuKambe
Titamvana ziwiri, ndikuthekesa ngini
Twee pano, palibe angadzalande

Nthawi zonse ndikakuwona, ngini yanga umayibanikisa
Maka maka ukayandikila,
nazo zonsezi (Osatengeka iwe)
Osada nkhawa (Osada nkhawa iwe)
Kusinkha za mawa (Zonse zamdziko izi)
Osasilira zinthu zodzasalira (Zonse zamdziko
Eeeeeh aahh
Make em follow you
Tula zonse ulinazo mwa yesu
Moyo uli mwa iye (Make em follow you)
Tula zonse ulinazo mwa yesu
Moyo uli mwa iye (Make em
ndatha Mtunda
Chonde osandifuna aaaa ye
Chonde osandifuna
Umakumbuka unanena
Ndimakumbuka nalira
Ndimakumbuka zonse eyah
Ndimakumbuka zonse eyaaa
Ngakhale amunene kuti ndi mambala
Ubwino wake ndauziwa eh

Amati zonse ndizotheka aise 
Amati zonse ndizotheka aise nabola golide
Amati zonse ndizotheka aise
Masewera palibe ine ndamanga lambaa udzisewera wekha ine ngwakumwamba
Uchimowo ndasiya zonse zija ndaleka nthawi yakwana tipite m'mwamba
Masewera
Chiyembekezo chodala chomwe tili nacho ife
Mwana munthu adza kudzatitenga ife kunka nafe m'mwambaa
Zakale zonse zapita zatsala za tsopano tili ndi
your sofa
Ine ndinagwa mchikondi koma chatha
Now you don't matter, usandithele data
Ain't this what you wanted
Ndakusiyila zonse
Now you're disturbing up
Tizipeleke kwa Ambuye watu Nyamalenga watu mwine zonse, atuitana akuti bwerani, bwerani ana musacedwe

Pomwe tuna badwa tunachokera kwa Ambuye,
Kunja kwacha, dzuwa latuluka. Anthu alowe komwe amasaka ndalama, eeh, koma tisananyamuke kumathokoza Mulungu mu zonse eeeh

Kuyamika mu zonse
you our needs)
Ndinu a mayi a Mulungu (You are mother of God)
Ndi amayi athu (And our mother too)
Zinthu zonse tizisowa (All those things we need)
yanga
Baba you supply
Zonse zomwe ndimasowa
Kuyesa kufotokoza
Ayi mpaka dzuwa litalowa
Everybody knows
Baba you supply
Zonse zomwe ndimasowa
Kuyesa
to me

Your actions speak louder
Maso pakamwa
Ndizo ziulura
Zonse wabisa
Your actions speak louder
Maso pakamwa
Ndizo ziulura
Zonse wabisa

Oky Ndamva
Zonse wakhala ukundichitira simmaiwala
Zose takhala tikukambilana sindiyiwala
Koma palibe ligileti inu achemwa
Palibe ligileti inu achemwa aah
Ine ndilibe
zofooka zanga you know
Nthawi zonse mundigwile pa nkono
I just don't wanna be a hypocrite

Muzabwelaso ngati mbala izi ndimadziwa
Chit'sime chamoyo kuchotsa
Love madness
Chikoka ngati magnet
Ndiku browser ngati internet
Ndiwe Princess, ndiwe Queen plus
Ndiwe wife, ndiwe zonse, nthawi zonse, Nyengo Zonse
Zonse Zanga (My every portion)

Verse One
Muthetse ludzu langa mchilala (quench my thirst from drought)
Chakudya changa mu njala (my food from
Yehova inu mulinane, Mundifungatirabe
Mundifungatirabe, munyengo zonse
Atate simundisiya
Verse1
Pamene njira yanga yagwa m'dima
Zatsogolo osadziwika
Inu
Ndafika kumuzi ndawana ndalama kulibe
Ndani andibela ine ndalama zanga
Inu amai ndani analowa munyumba manga
Zintu zanga zonse sindi ziona bwino
VERSE 1
 Nankala niganiza Pali vemumanichitila 
(mumanichitila)
Nivambili... Sininga pende

Chinikanga kuona vevimalenga mukazichita zonse izi...
kuwuka
Munandipatsa moyo wanu osatha
Chifundo chanu chinandi masula
Machimo anga mwafafaniza yeah
Ndi ntima wanga wonse
Ndi mphamvu zanga zonse
Ndizakweza
mwangodzadzana agwape
Osowa zochita busy kumangomwa mchape
Ati dollar zake zonse zija mesa mzakumidima
Osamakopeka nawo awo ngo nkhwima
Nanga mwanamwana ngati uyo

Discuss these Zonsé Lyrics with the community:

0 Comments

    We need you!

    Help build the largest human-edited lyrics collection on the web!

    Search for song lyrics by

    Genres »

    Styles »

    Browse Lyrics.com

    Quiz

    Are you a music master?

    »
    Which song was first sang by the band AJR?
    A I'm Ready
    B Way Less Sad
    C Bang!
    D Burn the House Down

    Free, no signup required:

    Add to Chrome

    Get instant explanation for any lyrics that hits you anywhere on the web!

    Free, no signup required:

    Add to Firefox

    Get instant explanation for any acronym or abbreviation that hits you anywhere on the web!