Tizipeleke (feat. Francis Bwalya)
Cosmas Chanda Bwalya
The easy, fast & fun way to learn how to sing: 30DaySinger.com
Tizipeleke kwa Ambuye watu Nyamalenga watu mwine zonse, atuitana akuti bwerani, bwerani ana musacedwe Pomwe tuna badwa tunachokera kwa Ambuye, anaika ncito zonse muli ife kusonyeza mpavu zake mwine wache, kusonyeza mpavu zake mwine wache Ntawi zonse pamene tiyenda paziko atouza kunkara bwino ndi anti, ndikubacitila zabwino ntawi zonse, kusonyeza ncito zake muli ife, kankalifwe Katie mdi ncito zatu sisikondweresa timakaika namankalodwe yatu. Ndepo cimalengesa na kucoka pamanso pamulungu, ndipo chimalengesa na kucoka pamanso pamulungu Nicifukwa cake tibwelere kuli Yesu, Nyamalenga wesu tionese mpavu zace, kuti tilamulile name tionese mpavu ndi Yesu muncito zatu ndimu kumpempera Pamene mayeso yatufikila Yesu atiuza tizatope kankale mavuto yatufikila Yesu tiuza tizatope
Become A Better Singer In Only 30 Days, With Easy Video Lessons!
Citation
Use the citation below to add these lyrics to your bibliography:
Style:MLAChicagoAPA
"Tizipeleke (feat. Francis Bwalya) Lyrics." Lyrics.com. STANDS4 LLC, 2024. Web. 21 Sep. 2024. <https://www.lyrics.com/lyric-lf/12427007/Cosmas+Chanda+Bwalya/Tizipeleke+%28feat.+Francis+Bwalya%29>.
Discuss the Tizipeleke (feat. Francis Bwalya) Lyrics with the community:
Report Comment
We're doing our best to make sure our content is useful, accurate and safe.
If by any chance you spot an inappropriate comment while navigating through our website please use this form to let us know, and we'll take care of it shortly.
Attachment
You need to be logged in to favorite.
Log In