We Outside
Achina Gattah Ase
The easy, fast & fun way to learn how to sing: 30DaySinger.com
Big tings a gwan Hustle ndi these tings are one Kufilla aire Ngati Bakili ndimapanga dollar zaine Am just here for fun Pretty girl kodi umwa chani Tenga Trans ID ngati ndasintha gender Lero nthumba muli khenge Sindupanga za budget ngati Gwengwe Uliwonse ukufunawo utenge Imwa mowa iwe tiyankhule ngende Swag kuyithila loko ngati Mbenjere All white ngati ndathawa kundende Ntafa lero nditha kuwusa mu Ntendere Fukwa vibe yalero nde ndi Sinati Ubwele wina Iwe umati Good vibe sizokokana ma shirt We outside koma utipeza nkati Lero it's a party party party Dollar ngati ndipa sate sate sate Tigona panja ngati guard guard guard We outside Iwe umati mati mati Lero it's a party party party Dollar ngati ndipa sate sate sate Tigona panja ngati guard guard guard We outside Iwe umati mati mati Bar man tabweletsa casket Nkazi ali mu suspense Angondiyan'gana ngati suspect Kanao O Kanao Wadzagula cider Wadzatulutsa card ndiku swiper Nkazitu ndiwa Chilembwe ngati Idah Rich Mamie angofuna ku viber Tsopano dear ndufuna ndikutrape Akuti osandiyitana deer ngati gwape Tadzingotenga mowa tiwuchape Nkaziyu ndiwachamba Zomwe akupanga zundibanda Ta payer rent koma tigona panjaaa Sinati Ubwele wina Iwe umati Good vibe sizokokana ma shirt We outside koma utipeza nkati Lero it's a party party party Dollar ngati ndipa sate sate sate Tigona panja ngati guard guard guard We outside Iwe umati mati mati Lero it's a party party party Dollar ndipa sate sate sate Tigona panja ngati guard guard guard We outside Iwe umati mati mati
Become A Better Singer In Only 30 Days, With Easy Video Lessons!
Citation
Use the citation below to add these lyrics to your bibliography:
Style:MLAChicagoAPA
"We Outside Lyrics." Lyrics.com. STANDS4 LLC, 2024. Web. 25 May 2024. <https://www.lyrics.com/lyric-lf/14173042/Achina+Gattah+Ase/We+Outside>.
Discuss the We Outside Lyrics with the community:
Report Comment
We're doing our best to make sure our content is useful, accurate and safe.
If by any chance you spot an inappropriate comment while navigating through our website please use this form to let us know, and we'll take care of it shortly.
Attachment
You need to be logged in to favorite.
Log In