Song parody of
We Outside
by Achina Gattah Ase
Here's where you get creative! Use our cool song parody creator to make a totally new musical idea and lyrics for the We Outside song by Achina Gattah Ase.
Simply click on any word to get rhyming words suggestion to use instead of the original ones. You may also remove or alter entire lines if needed — when you're done save your work and share it with our community — have fun!
Big tings a gwan
Hustle ndi these tings are one
Kufilla aire
Ngati Bakili ndimapanga dollar zaine
Am just here for fun
Pretty girl kodi umwa chani
Tenga
Trans ID ngati ndasintha gender
Lero nthumba muli khenge
Sindupanga za budget ngati Gwengwe
Uliwonse ukufunawo utenge
Imwa mowa iwe tiyankhule ngende
Swag kuyithila loko ngati Mbenjere
All white ngati ndathawa kundende
Ntafa lero nditha kuwusa mu Ntendere
Fukwa vibe yalero nde ndi
Sinati
Ubwele wina
Iwe umati
Good vibe sizokokana ma shirt
We outside koma utipeza nkati
Lero it's a party party party
Dollar ngati ndipa sate sate sate
Tigona panja ngati guard guard guard
We outside
Iwe umati mati mati
Lero it's a party party party
Dollar ngati ndipa sate sate sate
Tigona panja ngati guard guard guard
We outside
Iwe umati mati mati
Bar man tabweletsa casket
Nkazi ali mu suspense
Angondiyan'gana ngati suspect
Kanao O Kanao
Wadzagula cider
Wadzatulutsa card ndiku swiper
Nkazitu ndiwa Chilembwe ngati Idah
Rich Mamie angofuna ku viber
Tsopano dear ndufuna ndikutrape
Akuti osandiyitana deer ngati gwape
Tadzingotenga mowa tiwuchape
Nkaziyu ndiwachamba
Zomwe akupanga zundibanda
Ta payer rent koma tigona panjaaa
Sinati
Ubwele wina
Iwe umati
Good vibe sizokokana ma shirt
We outside koma utipeza nkati
Lero it's a party party party
Dollar ngati ndipa sate sate sate
Tigona panja ngati guard guard guard
We outside
Iwe umati mati mati
Lero it's a party party party
Dollar ndipa sate sate sate
Tigona panja ngati guard guard guard
We outside
Iwe umati mati mati
Big tings a gwan
Hustle ndi these tings are one
Kufilla aire
Ngati Bakili ndimapanga dollar zaine
Am just here for fun
Pretty girl kodi umwa chani
Tenga
Trans ID ngati ndasintha gender
Lero nthumba muli khenge
Sindupanga za budget ngati Gwengwe
Uliwonse ukufunawo utenge
Imwa mowa iwe tiyankhule ngende
Swag kuyithila loko ngati Mbenjere
All white ngati ndathawa kundende
Ntafa lero nditha kuwusa mu Ntendere
Fukwa vibe yalero nde ndi
Sinati
Ubwele wina
Iwe umati
Good vibe sizokokana ma shirt
We outside koma utipeza nkati
Lero it's a party party party
Dollar ngati ndipa sate sate sate
Tigona panja ngati guard guard guard
We outside
Iwe umati mati mati
Lero it's a party party party
Dollar ngati ndipa sate sate sate
Tigona panja ngati guard guard guard
We outside
Iwe umati mati mati
Bar man tabweletsa casket
Nkazi ali mu suspense
Angondiyan'gana ngati suspect
Kanao O Kanao
Wadzagula cider
Wadzatulutsa card ndiku swiper
Nkazitu ndiwa Chilembwe ngati Idah
Rich Mamie angofuna ku viber
Tsopano dear ndufuna ndikutrape
Akuti osandiyitana deer ngati gwape
Tadzingotenga mowa tiwuchape
Nkaziyu ndiwachamba
Zomwe akupanga zundibanda
Ta payer rent koma tigona panjaaa
Sinati
Ubwele wina
Iwe umati
Good vibe sizokokana ma shirt
We outside koma utipeza nkati
Lero it's a party party party
Dollar ngati ndipa sate sate sate
Tigona panja ngati guard guard guard
We outside
Iwe umati mati mati
Lero it's a party party party
Dollar ndipa sate sate sate
Tigona panja ngati guard guard guard
We outside
Iwe umati mati mati