Lyrics.com »

Search results for 'ntchito'

Yee yee! We've found 55 lyrics matching ntchito.

Year:


Filter by gender:

Lyrics:

Analembedwa ntchito mmmmmmm mmm mmm
Analembedwa ntchito mmmmmmm mmm mmm
Analembedwa ntchito mmmmmmm mmm mmm
Ankasakasaka daily mmm mmm
Anayipeza
moyo
Ndikapeze moyo inee ehhh
Ndikanali muutchimo
Ndikadali muutchimo mbuye munandifera mwachisomo chanu mwandipulumutsa ine
Osati kamba ka ntchito
Chifukwa Cha zochita za anthu ena

Moyo wanga aha
Njira zanga izi
Ndimafuna zizikhala za Yehova yekha
Thupi langa aha
Ntchito zanga izi
Ndimafuna ndizichita
been lying lying lying to you
I have been lying lying lying to you
Zoti ndine Nurse doctor ayee
Ndinkangokamba for you to accept
Ntchito yanga yeniyeni
kukwatira
Banja si Business banja si malonda
Awo muwauze awo
Asathamangile kukwatira
Banja si Business banja si malonda
Si NTChito

Ife tikumanenatu adona Inu
Hook
Dzuwa lawala pa phiri la Zomba
Aaaaah! Aaaaah! Aaaaah!
Tigwire ntchito
Dzuwa lawala pa phiri la Zomba
            Aaaaah! Aaaaah! Aaaaaah!
Experience ndipeza bwanji
Munthu ine school ndamaliza last year
Ntchito ndayisaka town mu
Kumangozungulilamo ngati ndine wa masiye
Nanga mpaka five years
ndakula nyumba ndapeza
Koma chondidabwitsa ndifuna  nditakhala mwana
Mabvuto achuluka ntchito kusowa
Koma rent angokweza ambuye ndipangeni mwana

Oh mwana
kunathetsedwa
1893 ikungotukukano skulu
1895 kunatulukira a Nguru
Anali mtundu wodabwitsa kuchokera ku Mozambique
Analolera kugwira ntchito kwa Nzungu opanda
the rest of my Life
Will you be mine
For the rest of my life
Yeah
Yeah
Will you be mine
Pala kopala lamala ntchito yamala dende lamala
Kuwuka nanjala
Mine
aliko Ku ghetto alikoso
Ku ntchito aliko ma copy cut ayi nono

Ukayamba geni ma guy akubwela ati nafeso
Moyo okopela  pamalawi  wanyanya tisanamepo
Haya Bengende

Wakondali Nde Khalidwe Lanji?
Kundipatsachi Chikondi Chanji?
Tsiku Lonse Mangokhalira Kuvula
Ntchito Yanga Nzikuveka Nde Udindo Wanji?
Ladzanso tsiku lakupula,
Lodalitsidwa ndi Mulunguyo;
Iye napuma ntchito zonsezo,
Ndipo afuna tipumulenso.
Iye napuma ntchito zonsezo,
Ndipo afuna
Atilemba ntchito abrazi...
Tayiphula game a Naz
Struggle tiyikhalira, tilemera
Pamenepa tinenepa zonse kunthazi.
Eyaditu broskie.
Talemera chonchi.
Koma
Malawi
I love malawi i love malaaawwii
Dziko lanthu lokongola anthu ake okongola
Zochepazo timagawana pamavuto sitithawana
Kugwira ntchito molimbika nsima
Aaaaaa
Big C

Uncle, Biggie

Ngati anthu ena ake amakukonda
Zindikira ena ake sakufuna
Ngati ena sangakhale opanda iwe
Kuli ena ati alibe ntchito
Thawizonse ndimanyadila
Oooh Mama
Inu nokha mumakwanila
Oooh Mama
Kumwamba
Dalisani amayi
Pa ntchito yabwino
Anagwila
Ooh yeah
Yeahh
Mwachikondi
On
He switched the channel of my life so now gotta Press On
Emmanuel no TV, Zapadziko zonse zilibe ntchito that's no CV
Check my story and my DP
Shirt ndi
Nde kulikonse komwe nzapita
I'll represent CHRIST to the fullest wazizur?

Yeah
Ambuye anati mfana wopanda ntchito you need some company
Mu Aiguputo si
Chilengedwe chibweletsa chuma
Komanso chikongolesa dziko
Tisakwatilitse ana ang'ono
Tiwalimbikitse sukulu
Tilimbikire kugwira ntchito
Tipange ulimi wamakono
Ndilibenazo ntchito
Akapasule akambe akambe
Adzakhala chete
Tidzawaleka
Tiwadzawaleka aha

Bekumele simubong'umdali 
Kumele simubonge. 
Uyabona ngelendlela
You'll be a testimony yeah (You'll testify)
You'll testify
What the Lord has done

Usiku ndi usana osagona
Kalilikiliki kusaka ntchito
Monday to Friday
Wakutsina khutu ndi mnasi, I'm just preaching
Tigwire ntchito ya Yehova tikalandire corona
No matenda, eya no matenda

Uwu ndi utumiki
As long as you got
tawuka Makora
Kaya yuko mwafumako ayi lero Koma bola
Ukuu, ndiye kumpoto yapa mwafika Pa Jenda
Tikambiraneno va ntchito kweni Tiyambe agenda
Ati ayi

Discuss these ntchito Lyrics with the community:

0 Comments

    We need you!

    Help build the largest human-edited lyrics collection on the web!

    Search for song lyrics by

    Genres »

    Styles »

    Browse Lyrics.com

    Quiz

    Are you a music master?

    »
    Which song was discussed by the characters in the movie Reservoir Dogs?
    A Fool for love
    B Like a virgin
    C Across 110th Street
    D Coconut

    Free, no signup required:

    Add to Chrome

    Get instant explanation for any lyrics that hits you anywhere on the web!

    Free, no signup required:

    Add to Firefox

    Get instant explanation for any acronym or abbreviation that hits you anywhere on the web!