Chitelire
Madah Khauya
Struggling with Chitelire? Become a better singer in 30 days with these videos!
Akuchimuna nkesa munkanena motumbwa Akuchikazi mesa munkanena monyang'wa Kuti tsiku la ukwati ndithu mudzatimva madzi Heh Lero mwangoti chete tavinani tione A ya ya ya ya ya Akuchimuna nkesa munkanena motumbwa inuyo Akuchikazi mesa munkanena monyada inuyo Kuti tsiku la ukwati ndithu mudzatimva m'bebe Heh Lero mwangoti chete tavinani tione A ya ya ya ya ya ya Chite chite chite chite chitelire Chite chite chite chite chitelire Chite chite chite chite chitelire Eya Chalira tsiku laukwati Chite chite chite chite chitelire Chite chite chite chite chitelire Chite chite chite chite chitelire Eya Chalira tsiku laukwati A ya ya ya ya ya ya ya ya ya ya ya Akuchimuna mesa munkanena mwathamo Kuti paukwati ng'ombe mbuzi mudzapha nokha Nanga bwanji mukukanika ndikupha ndi nkhuku zomwe Heh Takhumudwa nanu mwatichititsa manyazi A ya ya ya ya Akuchimuna mesa munkanena mwathamo inuyo Kuti paukwati ng'ombe mbuzi mudzapha nokha inuyo Nanga bwanji mukukanika ndikuzinga n'nkhuku zomwe Heh Takhumudwa nanu mwatichititsa manyazi A ya ya ya ya Chite chite chite chite chitelire Chite chite chite chite chitelire Chite chite chite chite chitelire Eya Chalira tsiku laukwati Chite chite chite chite chitelire Chite chite chite chite chitelire Chite chite chite chite chitelire Eya Chalira tsiku laukwati A ya ya ya ya ya ya ya ya ya ya ya Akuchikazi mesa munkanena modzimva Kuti mudzaphika thobwa lokwanila tonsefe Nanga bwanji ena akutitu lawapelewera Takhumudwa nanu mwatichititsa manyazi A ya ya ya ya Akuchikazi mesa munkanena mwathamo inuyo Kuti mudzaphika thobwa lokwanila tonsefe inuyo Nanga bwanji ena akutitu lawapelewera Takhumudwa nanu mwatichititsa manyazi A ya ya ya ya ya ya ya ya Chite chite chite chite chitelire Chite chite chite chite chitelire Chite chite chite chite chitelire Eya Chalira tsiku laukwati Chite chite chite chite chitelire Chite chite chite chite chitelire Chite chite chite chite chitelire Eya Chalira tsiku laukwati A ya ya ya ya ya ya ya ya ya ya ya Tiye Tiye Tiye A ya ya ya ya ya ya ya ya ya ya ya Tiye Tiye Tiye Chitelire Chitelire A ya ya ya ya Ati chalila A ya ya ya ya Chitelire Chitelire Chitelire Chalila Ati chalila Chitelire A ya ya ya ya Chitelire A ya ya ya ya ya Ati chalila
Watch: New Singing Lesson Videos Can Make Anyone A Great Singer
Citation
Use the citation below to add these lyrics to your bibliography:
Style:MLAChicagoAPA
"Chitelire Lyrics." Lyrics.com. STANDS4 LLC, 2024. Web. 18 Jun 2024. <https://www.lyrics.com/lyric-lf/8216034/Madah+Khauya/Chitelire>.
Discuss the Chitelire Lyrics with the community:
Report Comment
We're doing our best to make sure our content is useful, accurate and safe.
If by any chance you spot an inappropriate comment while navigating through our website please use this form to let us know, and we'll take care of it shortly.
Attachment
You need to be logged in to favorite.
Log In