Miyala
Cozizwa
Struggling with Miyala? Become a better singer in 30 days with these videos!
Hey Hey Heeeyah aye Heeeyah aye Pakamwa pomwe ndiimbira nyimbo yanga Tsiku lina ndithu yahwe adzandifunsa (Funsa funsa funsa) Pakamwa n'nakupatsa N'chifukwa chani unkaphyozera zingombingo? Miyendo yomwe uvinira nyimbo yangayi Tsiku lina ndithu Yahwe adzakufunsa (Funsa funsa funsa) Miyendo nnakupatsa Ona unkapalasila kokabera anthu? Koma ine, koma ine Ine ndinsembe yamatamando Koma ine, koma ine Ine ndinsembe yamatamando Musandiuze ndikhale phee Apo bii Miyala isokosa (Miyala isokosa) Eeeeh sindikhala phee Apo bii Miyala isokosa pano (Miyala isokosa) Ndikuti shaa Miyala isokosa pano (Miyala isokosa) Isokosa pano (Miyala isokosa) Ndikuti eeh Miyala isokosa pano (Miyala isokosa) Isokosa pano (Miyala isokosa) Ndikuti shaa Miyala ilalata pano (Miyala ilalata) Ilalata pano (Miyala ilalata) Ndikuti woh Miyala ilalata pano (Miyala ilalata) Miyala ilalata pano (Miyala ilalata) Heey Kuli achina mbuzi Kuli achina ng'ombe Kuli achina makoswe Kuli achina mbalame Kuli achina mphaka Kuli achina agalu Kuli achina ntchentche Kuli achina ngumbi Ine ndimachita chidwi ndi mwala Poti mwala ulibe pakamwa Koma kudzaiyang'ana mbuzi, ili kukamwa yasa Koma nkadzamuyang'ana galu, naye alikukamwa yasa (Eeeh) Kudzaiyang'ana mbewa, nayo ili kukamwa yasamuleni Koma ngati mau akunena, mwala udzaimba nyimbo kuli bwanji makoswe Ngati mau akunena, mwala udzaimba nyimbo kuli bwanji mbewa Musandiuze ndikhale phee Inu apo bii Miyala isokosa (Miyala isokosa) Eeeeh ndati sindikhala phee Apo bii Miyala isokosa pano (Miyala isokosa) Ndikuti woh Miyala isokosa pano (Miyala isokosa) Miyala isokosa pano (Miyala isokosa) Ndikuti woh Miyala isokosa pano (Miyala isokosa) Miyala isokosa pano (Miyala isokosa) Ndikuti shaa Miyala iyankhula pano Miyala iyankhula pano Ehhh Miyala ichezapo pano Miyala ichezapo pano Ndikuti woh Miyala ilalata pano (Miyala ilalata) Miyala ilalata pano (Miyala ilalata) Miyala ilalata pano (Miyala ilalata) Miyala ilalata pano (Miyala ilalata) Kuli achina mbewa Kuli achina nkhuku Kuli achina mphemvu Kuli achina gwafa Kuli achina mbatata Kuli achina khoswe Kuli achina nkhuku Eh ine ndimtama tsiku lonse Ndimtama tsiku lonse ineyo Ndati ndimtama tsiku lonse Ine ndimtama tsiku lonse Ndimtama tsiku lonse Ndimtama tsiku lonse Eeeeh ndati ndimtama tsiku lonse Ine ndimtama tsiku lonse
Watch: New Singing Lesson Videos Can Make Anyone A Great Singer
Citation
Use the citation below to add these lyrics to your bibliography:
Style:MLAChicagoAPA
"Miyala Lyrics." Lyrics.com. STANDS4 LLC, 2024. Web. 17 Jun 2024. <https://www.lyrics.com/lyric-lf/4169016/Cozizwa/Miyala>.
Discuss the Miyala Lyrics with the community:
Report Comment
We're doing our best to make sure our content is useful, accurate and safe.
If by any chance you spot an inappropriate comment while navigating through our website please use this form to let us know, and we'll take care of it shortly.
Attachment
You need to be logged in to favorite.
Log In