Nkono

Kelvin Sings

0 fans

Kelvin Sings


2:49
#1

 Become A Better Singer In Only 30 Days, With Easy Video Lessons!

Alright Alright Alright
See we go rock again boy!
Ndani angawongole zomwe mwapinda
Kuulula zomwe mwabisa
Ndani angabwenzeretse zomwe mwasintha
Palibe!
Za inu sindikusowa ku-funsa
Ndine mboni ya moto olusa
Chipani cholamula nkhondo kwa otsutsa
Chuma kwa anzeru umphawi kwa opusa
Woosaaah!!!
Dekha uwone
Amapanga za ine ndili gone
Ngati amasamalira zomela
Why would i worry?
Why why why why?
Tingadutse muzikhomo aye
khomo aye
Koma Yesu Ali m'momo aye
M'momo aye
Andikuta ndi chisomo aye
Somo aye
Ndicho chindigwira nkono aye
Nkono aye
Oh nananana!
Chisomo aye Chisomo
Mumandigwira nkono
Chisomo aye Chisomo
Simundisiya m'momo
Zikomo aye Zikomo
Mumandigwira nkono
Chisomo aye Chisomo
Simundisiya m'momo
Ndine ochepekedwa iye ndi odzadza
Nyonga zikachepa amakankha
Kukankha ngini yanga amatsata
Yake ija ija ana ake amajaja!
Ndikamakhala ndikamadzuka ndikamayenda
Ndimadziwa chilichonse chili m'manja mwa Namalenga
Chilamulo chake pena ndikazemba
Chisomo chake chidzadza denga denga
Dekha uwone
Amapanga za ine ndili gone
Ngati amasamalira zomela
Why would i worry?
Why why why why?
Tingadutse muzikhomo aye
khomo aye
Koma Yesu Ali mmomo aye
M'momo aye
Andikuta ndi chisomo aye
Somo aye
Ndicho chindigwira nkono aye
Nkono aye
Oh nananana!
Chisomo aye Chisomo
Mumandigwira nkono
Chisomo aye Chisomo
Simundisiya m'momo
Zikomo aye Zikomo
Mumandigwira nkono
Chisomo aye Chisomo
Simundisiya m'momo

 Watch: New Singing Lesson Videos Can Make Anyone A Great Singer

Written by: Kelvin Zalimba

Lyrics © O/B/O DistroKid

Lyrics Licensed & Provided by LyricFind

Discuss the Nkono Lyrics with the community:

0 Comments

    Citation

    Use the citation below to add these lyrics to your bibliography:

    Style:MLAChicagoAPA

    "Nkono Lyrics." Lyrics.com. STANDS4 LLC, 2024. Web. 28 May 2024. <https://www.lyrics.com/lyric-lf/13700076/Kelvin+Sings/Nkono>.

    Missing lyrics by Kelvin Sings?

    Know any other songs by Kelvin Sings? Don't keep it to yourself!

    Browse Lyrics.com

    Quiz

    Are you a music master?

    »
    What is the name of the person who performed the song "Never Gonna Give You Up"?
    A Rick Ashley
    B Rick Assley
    C RickRoll
    D Rick Astley

    Free, no signup required:

    Add to Chrome

    Get instant explanation for any lyrics that hits you anywhere on the web!

    Free, no signup required:

    Add to Firefox

    Get instant explanation for any acronym or abbreviation that hits you anywhere on the web!

    Kelvin Sings tracks

    On Radio Right Now

    Loading...

    Powered by OnRad.io


    Think you know music? Test your MusicIQ here!