MAPOKOSO (Bonus track)

KIOSK MLW

0 fans

KIOSK MLW


2:48

 Become A Better Singer In Only 30 Days, With Easy Video Lessons!

Greatness
I asked her kodi umangofuna tiziyambana everyday
Utha kupita I don't care anyway
Ukangobwela kundivutitsa daily
Zimakuwaza zopha vibe yaine
Ukangobwela mapokoso
Olo ma neighbor sagona pa line ponse
Mbili yako inanveka paliponse
Kukulangiza sunza umamenyaso ankhoswe
[lets go]
Subweletsa chikondi ukubweletsa phokoso
Pa line mtendele wasowaponso
Ndanva kuti alendo ukumawathangitsa
Sumandinvela ndizomwe umalakwitsa
Ndikamakuyankhula ukumaima ma stanz
Ukudzinva zimphanvu ukudzinva u swazi
Utha kumapita yeayea ndikhala fine
Leave me in piece ndatopa ndizi nkhani
I asked her kodi umangofuna tiziyambana everyday
Utha kupita I don't care anyway
Ukangobwela kundivutitsa daily
Zimakuwaza zopha vibe yaine
Ukangobwela mapokoso
Olo ma neighbor sagona pa line ponse
Mbili yako inanveka paliponse
Kukulangiza sunza umamenyaso ankhoswe
[lets go]
Iwe philomina ndikuona uku trippa
Kuvuta umavuta but its getting out of hand
Bwanji osandiuza ngati wapeza wina
Kufuna ndimafuna koma zandikanika
Ukufunano chani?
Zonse watenga
You tryna change my plan?
Kapena wapenga?
Sizikutheka pano ndalimba mtima
Ndizingopita panopa sinduima
I asked her kodi umangofuna tiziyambana everyday
Utha kupita I don't care anyway
Ukangobwela kundivutitsa daily
Zimakuwaza zopha vibe yaine
Ukangobwela mapokoso
Olo ma neighbor sagona pa line ponse
Mbili yako inanveka paliponse
Kukulangiza sunza umamenyaso ankhoswe
[Lets go]
Purple made it

 The easy, fast & fun way to learn how to sing: 30DaySinger.com

Written by: Benjamin Madeya, Ruben Mtupanyama

Lyrics © DistroKid

Lyrics Licensed & Provided by LyricFind

Discuss the MAPOKOSO (Bonus track) Lyrics with the community:

0 Comments

    Citation

    Use the citation below to add these lyrics to your bibliography:

    Style:MLAChicagoAPA

    "MAPOKOSO (Bonus track) Lyrics." Lyrics.com. STANDS4 LLC, 2024. Web. 24 Sep. 2024. <https://www.lyrics.com/lyric-lf/12364797/KIOSK+MLW/MAPOKOSO+%28Bonus+track%29>.

    Missing lyrics by KIOSK MLW?

    Know any other songs by KIOSK MLW? Don't keep it to yourself!

    Browse Lyrics.com

    Quiz

    Are you a music master?

    »
    Who played the guitar solo in Michael Jackson's "Beat It"?
    A Jimi Hendrix
    B Keith Richards
    C Eddie Van Halen
    D Angus Young

    Free, no signup required:

    Add to Chrome

    Get instant explanation for any lyrics that hits you anywhere on the web!

    Free, no signup required:

    Add to Firefox

    Get instant explanation for any acronym or abbreviation that hits you anywhere on the web!

    KIOSK MLW tracks

    On Radio Right Now

    Loading...

    Powered by OnRad.io