BONA
JEG Tellem
Struggling with BONA? Become a better singer in 30 days with these videos!
Yahman yah Tellem Zomwe ndikumaona Dziko li linagona Satana Pano anangolowa paliponse kulimeza ngati chi Ng'ona Akufalitsa ti mabodza Angofuna kuti pomboneza Eti uthenga wabho ena ati ndizanyasi mhhu mukumanyoza ah ah Koma sindingasiye Ku praiser ine praiser ine eh Ndimamutsata Yahweh ndipo ndimamupembeza ine mbeza ine hey Masten aziziwa mawu awo mawasungabe sungabe eh Uzikonda Chauta Namalenga pokusunga iwe sunga iwe hey Devil yo kumubona ahah Mpaka akumagoma ahah Wakumana ndi CHIPHONA ah SUNDIKOPA kopa ase Devil yo kumubona mmhu Mpaka akumagoma mmhu Wakumana ndi CHIPHONA SUNDIKOPA kopa ase Ey yeah yah Ndipo sinkuopa ase Ey yeeh yah SUNDIKOPA kopa ase Ey yeah yah Ndipo sinkuopa ase Ey yeah yah Kuyimba nako kukayamba kukoma Satana naye nde saku mapuma Akusaka tinjira atikole tizimupopa koma wagoma Nyengo zaka nazo zikayamba kusintha Ndipamene akufuna ndizifuntha Kenako nkhale desperate ndimutsate eti sindipanga izi ataaa Koma sindingasiye Ku praiser ine praiser ine eh Ndimamutsata Yahweh ndipo ndimamupembeza ine mbeza ine hey Masten aziziwa mawu awo mawasungabe sungabe eh Uzikonda Chauta Namalenga pokusunga iwe sunga iwe hey Devil yo kumubona ah ah Mpaka akumagoma ah ah Wakumana ndi CHIPHONA ah SUNDIKOPA kopa ase Devil yo kumubona mmhu Mpaka akumagoma mmhuu Wakumana ndi CHIPHONA SUNDIKOPA kopa ase Ey yeay yah Ndipo sinkuopa ase Ey yeah yah SUNDIKOPA kopa ase Ey yeah yah Ndipo sinkuopa ase Ey yeah yah
The easy, fast & fun way to learn how to sing: 30DaySinger.com
Citation
Use the citation below to add these lyrics to your bibliography:
Style:MLAChicagoAPA
"BONA Lyrics." Lyrics.com. STANDS4 LLC, 2024. Web. 30 May 2024. <https://www.lyrics.com/lyric-lf/12235495/JEG+Tellem/BONA>.
Discuss the BONA Lyrics with the community:
Report Comment
We're doing our best to make sure our content is useful, accurate and safe.
If by any chance you spot an inappropriate comment while navigating through our website please use this form to let us know, and we'll take care of it shortly.
Attachment
You need to be logged in to favorite.
Log In