Mukhalebe Okhulupirika

The Dwellers MW

0 fans

The Dwellers MW


3:45

 Become A Better Singer In Only 30 Days, With Easy Video Lessons!

Namondweeetu angakuleee
(Mukhalebe Okhulupirika)
Namondweeetu angakuleee
(Mukhalebe Okhulupirika)

Zilibe kanthu moyo kuvuta mukhalebe  okhulupirika
Zilibe kanthu mulibe ndalama mubwezebe chachikhumi
Zilibe kanthu moyo kuvuta mukhalebe  okhulupirika
Zilibe kanthu mulibe ndalama mubwezebe chachikhumi

Zambiritu zidzayenda
(Mukamtsatira Mulungu)
Inu zambiritu zidzayendaaa
(Mukamtsatira Mulungu)

Zilibe kanthu moyo kuvuta mukhalebe  okhulupirika
Zilibe kanthu mulibe ndalama mubwezebe chachikhumi

Zilibe (kanthu moyo kuvuta mukhalebe  okhulupirika)
Zilibe kanthu mulibe ndalama mubwezebe chachikhumi

Zilibe (kanthu moyo kuvuta mukhalebe  okhulupirika)
Zilibe kanthu mulibe ndalama mukhalebe okhulupirikaaaa

 Watch: New Singing Lesson Videos Can Make Anyone A Great Singer

Written by: Benjamin Mtukumila, Blessings Msiska, Glory Majolo, Mphatso Chipandula, Thelma Chinyama, Thokozile Msiska

Lyrics © DistroKid

Lyrics Licensed & Provided by LyricFind

Discuss the Mukhalebe Okhulupirika Lyrics with the community:

0 Comments

    Citation

    Use the citation below to add these lyrics to your bibliography:

    Style:MLAChicagoAPA

    "Mukhalebe Okhulupirika Lyrics." Lyrics.com. STANDS4 LLC, 2024. Web. 25 Jun 2024. <https://www.lyrics.com/lyric-lf/11548915/The+Dwellers+MW/Mukhalebe+Okhulupirika>.

    Missing lyrics by The Dwellers MW?

    Know any other songs by The Dwellers MW? Don't keep it to yourself!

    Browse Lyrics.com

    Quiz

    Are you a music master?

    »
    Robert Allen Zimmerman is better known as?
    A Bob Seger
    B Bob Geldof
    C Bob Dylan
    D Rob Zombie

    Free, no signup required:

    Add to Chrome

    Get instant explanation for any lyrics that hits you anywhere on the web!

    Free, no signup required:

    Add to Firefox

    Get instant explanation for any acronym or abbreviation that hits you anywhere on the web!

    The Dwellers MW tracks

    On Radio Right Now

    Loading...

    Powered by OnRad.io


    Think you know music? Test your MusicIQ here!