Mpunga
Guntolah
Watch: New Singing Lesson Videos Can Make Anyone A Great Singer
Sitonse tikufuna chibwenzi Sitonse tingakhale m'chibwezi Si tonse tikulilira chikondi iii Si tonse tikufuna chikondi Ife tingofuna mpunga wa nyama Mpunga wa nyama Ife tingofuna mpunga wa nyama Mpunga wa nyama Ukavuta wa soya pieces kapena chipisi Ukavuta wa soya pieces kapena chipisi Ife tingofuna mpunga wa nyama Mpunga wa nyama Ife tingofuna mpunga wa nyama Mpunga wa nyama sitikufuna chikondi mpunga wa nyama Sindikufuna chikondi no no no no no Sindikufuna kuzanong'oneza bondo ndufuna ka mpunga ma pang'ono Ka nyama pang'ono Ndufuna kumwako ka sobo ka beer pang'ono Ine ndingofuna kuutunga Chomwe ndi kufuna ndi mpunga Mpunga wa nyama Ife tingofuna mpunga wa nyama Mpunga wa nyama Ife tingofuna mpunga wa nyama Mpunga wa nyama Ukavuta wa soya pieces kapena chipisi Ukavuta wa soya pieces kapena chipisi Ife tingofuna mpunga wa nyama Mpunga wa nyama Ife tingofuna mpunga wa nyama Mpunga wa nyama Sitikufuna chikondi mpunga wa nyama Mpunga wa nyamaa Mpunga wa nyamaa Mpunga wa nyamaa Mpunga wa nyamaa
Struggling with Mpunga? Become a better singer in 30 days with these videos!
Citation
Use the citation below to add these lyrics to your bibliography:
Style:MLAChicagoAPA
"Mpunga Lyrics." Lyrics.com. STANDS4 LLC, 2024. Web. 24 Sep. 2024. <https://www.lyrics.com/lyric-lf/10585971/Guntolah/Mpunga>.
Discuss the Mpunga Lyrics with the community:
Report Comment
We're doing our best to make sure our content is useful, accurate and safe.
If by any chance you spot an inappropriate comment while navigating through our website please use this form to let us know, and we'll take care of it shortly.
Attachment
You need to be logged in to favorite.
Log In