Idzani Mzimu Olenga (Chichewa Hymn 43)
Edgar Kapiza Bayani
The easy, fast & fun way to learn how to sing: 30DaySinger.com
Idzani Mzimu Olenga (Come Holy Spirit) Mulowe mitima mwathu (Enter into our hearts) Ndikuyidzadzitsa ndithu (And fill them) Ndi chaulere cha kumwamba (With Heavenly Grace) Mudza kutisekeretsa (You bring joy unto us) Potininkha Moyo wanu (By giving us your heavenly life) Ndi chikondi chachikulu (Shared with unconditional love) Ndi zonse zina tisowa (And all that we need) Mphatso zanu zozizwitsa (Your miraculous gifts) Muziyike mtima mwathu (Unto our hearts fill them) Zitidziwitse Mulungu (To help us know God) Ndi ntchito zake zokoma (And His wondrous works) Mutionjezele nzeru (Grant us wisdom) Ndichikondi mtima mwathu (And fill our hearts with love) Ndiponso ndi mphamvu zanu (And with your mightiness) Mulimbitse thupi lathu (Strengthen our frail bodies) Mudzathawitse Satana (Keep the devil away) Ndi zoyipa zake zonse (And all his evil ways) Kuti tipeze mtendere (So that in peace we dwell) Pakutsata Inu nokha (And serve only you) Tilemekeze Atate (Praise to God the Father) Ndi Mwana ouka m'manda (And to son who rose from the dead) Ndi Mzimu osangalatsa (And to the Spirit who gladdens us) Lero ndi masiku onse (Today and for ever more)
Become A Better Singer In Only 30 Days, With Easy Video Lessons!
Citation
Use the citation below to add these lyrics to your bibliography:
Style:MLAChicagoAPA
"Idzani Mzimu Olenga (Chichewa Hymn 43) Lyrics." Lyrics.com. STANDS4 LLC, 2024. Web. 26 May 2024. <https://www.lyrics.com/lyric-lf/7092277/Edgar+Kapiza+Bayani/Idzani+Mzimu+Olenga+%28Chichewa+Hymn+43%29>.
Discuss the Idzani Mzimu Olenga (Chichewa Hymn 43) Lyrics with the community:
Report Comment
We're doing our best to make sure our content is useful, accurate and safe.
If by any chance you spot an inappropriate comment while navigating through our website please use this form to let us know, and we'll take care of it shortly.
Attachment
You need to be logged in to favorite.
Log In