Lyrics:
Ndafika kumuzi ndawana ndalama kulibe
Ndani andibela ine ndalama zanga
Inu amai ndani analowa munyumba manga
Zintu zanga zonse sindi ziona bwino
anu anangochoka alamu anu
Ayiwala zonse, tinakambilana zija
Ayiwala zonse, tinalambilana zina eish
Ayiwala zonse, ndinawapangila zija
Ayiwala zonse
Andiveka Yesu daily
Zanga zose tayali
Ndayiwala hardship
Kufewa daily
Zonse zanga khengi
Kucheza pa deni ndi sisi
Kutenga photo Hd
Nkhope kuwala nyali
Ine
chasefukira
Moyo wanga unasintha
Mtima wanga kuyamika
Ndizovuta kunena
M'mene m'mandikondera
Mwandimasula ku nsinga
Mtima wanga kuyamika
Ndinu zonse zanga
Kunja kwacha, dzuwa latuluka. Anthu alowe komwe amasaka ndalama, eeh, koma tisananyamuke kumathokoza Mulungu mu zonse eeeh
Kuyamika mu zonse
Tizipeleke kwa Ambuye watu Nyamalenga watu mwine zonse, atuitana akuti bwerani, bwerani ana musacedwe
Pomwe tuna badwa tunachokera kwa Ambuye,
Masewera palibe ine ndamanga lambaa udzisewera wekha ine ngwakumwamba
Uchimowo ndasiya zonse zija ndaleka nthawi yakwana tipite m'mwamba
Masewera
Yehova inu mulinane, Mundifungatirabe
Mundifungatirabe, munyengo zonse
Atate simundisiya
Verse1
Pamene njira yanga yagwa m'dima
Zatsogolo osadziwika
Inu
tate wadziko lonse
ndiimba matamando
ndinu oyera mnjira zonse
inu mundiyang'anira
masiku amoyo wanga
back to chorus
Ukamati Zako Zonse Ndi Ine eeh
Zanga Zonse Ndizako
Paja Unati Singandisiye eeh
Supanga Chipako
Ndiwe Moyo Wanga Unawina aah
Nkhope yako Imakana Tsinya aah
ndatha Mtunda
Chonde osandifuna aaaa ye
Chonde osandifuna
Umakumbuka unanena
Ndimakumbuka nalira
Ndimakumbuka zonse eyah
Ndimakumbuka zonse eyaaa
tikuKambe
Titamvana ziwiri, ndikuthekesa ngini
Twee pano, palibe angadzalande
Nthawi zonse ndikakuwona, ngini yanga umayibanikisa
Maka maka ukayandikila,
Chiyembekezo chodala chomwe tili nacho ife
Mwana munthu adza kudzatitenga ife kunka nafe m'mwambaa
Zakale zonse zapita zatsala za tsopano tili ndi
Eeeeeh aahh
Make em follow you
Tula zonse ulinazo mwa yesu
Moyo uli mwa iye (Make em follow you)
Tula zonse ulinazo mwa yesu
Moyo uli mwa iye (Make em
mtendere
Ukayandikira iwe ndimva kukoma
Sindidzamkonda wina ndapeza iwe
Mphatso ya Mulungu
Umandiyatsa moto mtima
Umandichotsa nkhawa zonse
Sinditha kukhala
na mwezi
Ni ona ukulu wanu
Ukulu wanu
Ndamona mulonga
Milundu nyikajulu
Yonse itondeye bupati wenu ,bupati wenu
Zonse munalenga ,Zonse
to me
Your actions speak louder
Maso pakamwa
Ndizo ziulura
Zonse wabisa
Your actions speak louder
Maso pakamwa
Ndizo ziulura
Zonse wabisa
Oky Ndamva
nazo zonsezi (Osatengeka iwe)
Osada nkhawa (Osada nkhawa iwe)
Kusinkha za mawa (Zonse zamdziko izi)
Osasilira zinthu zodzasalira (Zonse zamdziko
yanga
Baba you supply
Zonse zomwe ndimasowa
Kuyesa kufotokoza
Ayi mpaka dzuwa litalowa
Everybody knows
Baba you supply
Zonse zomwe ndimasowa
Kuyesa
Munkakati ndine woipa
Nthakati wachabechabe
Mwanena zaine mwatopa
Mwaimbaimba zaine mwatopa
Zoipa zanga zonse mwaimba
Asakudziwa ndani
Munkati ndine
nkamfuna apezeka.
Nkamfuna Yesu ndiwamphamvu, nkhawa zonse andisenzera.
Nandipatsa chimwemwe chake, nkamfuna apezeka.
Nkamfuna Apezeka nkamfuna apezeka
you our needs)
Ndinu a mayi a Mulungu (You are mother of God)
Ndi amayi athu (And our mother too)
Zinthu zonse tizisowa (All those things we need)
Nkhalango
Nthawi zonse ndinu mayi odala..
Chorus (X2)
Mayiii. Malawi
Mayiii Malawi
Mayiii Malawi
Mayiii Malawi
Mayiii Malawi
Mayiii Malawi
inu
Izi ndimadziwa ine e
Zoti mmandikonda ine
Izi ndimadziwa ine
Zoti ndinu wa mphamvu inu
Izi ndimadziwa ine e
Mmandikonda inu Mbuye
Nthawi zonse
Discuss these zonse Lyrics with the community:
Report Comment
We're doing our best to make sure our content is useful, accurate and safe.
If by any chance you spot an inappropriate comment while navigating through our website please use this form to let us know, and we'll take care of it shortly.
Attachment
You need to be logged in to favorite.
Log In